-
Yesaya 57:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Mphepo idzaulutsa mafano onsewo
Ndipo mpweya udzawakankhira kutali,
Koma munthu amene amathawira kwa ine adzalandira dziko
Ndipo adzatenga phiri langa loyera kukhala lake.+
-