Yesaya 57:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno wina adzanena kuti, ‘Konzani msewu! Konzani msewu! Konzani njira!+ Chotsani chopinga chilichonse panjira ya anthu anga.’” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 57:14 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2023, ptsa. 16-17 Yesaya 2, ptsa. 270, 272-273
14 Ndiyeno wina adzanena kuti, ‘Konzani msewu! Konzani msewu! Konzani njira!+ Chotsani chopinga chilichonse panjira ya anthu anga.’”