Yesaya 57:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ine ndinakwiya chifukwa cha machimo amene ankachita pofuna kupeza phindu mwachinyengo,+Choncho ndinamulanga, ndinabisa nkhope yanga ndipo ndinakwiya. Koma iye anapitiriza kuyenda ngati wopanduka,+ ankangotsatira zofuna za mtima wake. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 57:17 Yesaya 2, ptsa. 271-272
17 Ine ndinakwiya chifukwa cha machimo amene ankachita pofuna kupeza phindu mwachinyengo,+Choncho ndinamulanga, ndinabisa nkhope yanga ndipo ndinakwiya. Koma iye anapitiriza kuyenda ngati wopanduka,+ ankangotsatira zofuna za mtima wake.