Yesaya 58:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Iye anandiuza kuti: “Fuula mwamphamvu! Usabweze mawu. Kweza mawu ako ngati lipenga. Uza anthu anga za kupanduka kwawo.+A nyumba ya Yakobo uwauze machimo awo. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 58:1 Yesaya 2, ptsa. 276-277
58 Iye anandiuza kuti: “Fuula mwamphamvu! Usabweze mawu. Kweza mawu ako ngati lipenga. Uza anthu anga za kupanduka kwawo.+A nyumba ya Yakobo uwauze machimo awo.