Yesaya 58:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ‘Nʼchifukwa chiyani simukuona pamene tikusala kudya?+ Ndipo nʼchifukwa chiyani simukuona tikamadzisautsa?’+ Chifukwa chakuti pa tsiku lanu losala kudya mumachita zofuna zanu,*Ndipo mumapondereza antchito anu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 58:3 Nsanja ya Olonda,4/1/2009, tsa. 29 Yesaya 2, ptsa. 279-280 Galamukani!,3/8/1995, tsa. 9
3 ‘Nʼchifukwa chiyani simukuona pamene tikusala kudya?+ Ndipo nʼchifukwa chiyani simukuona tikamadzisautsa?’+ Chifukwa chakuti pa tsiku lanu losala kudya mumachita zofuna zanu,*Ndipo mumapondereza antchito anu.+