Yesaya 58:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mukamasala kudya zotsatira zake zimakhala kukangana komanso ndewu,Ndipo mumamenya anzanu mwankhanza ndi zibakera.* Simungamasale kudya ngati mmene mukuchitira panopa nʼkumayembekezera kuti mawu anu amveka kumwamba. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 58:4 Yesaya 2, ptsa. 279-280
4 Mukamasala kudya zotsatira zake zimakhala kukangana komanso ndewu,Ndipo mumamenya anzanu mwankhanza ndi zibakera.* Simungamasale kudya ngati mmene mukuchitira panopa nʼkumayembekezera kuti mawu anu amveka kumwamba.