-
Yesaya 58:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kodi kusala kudya kumene ine ndinakulamulani nʼkumeneku?
Kodi likhale tsiku loti munthu azidzisautsa,
Kuti aziweramitsa mutu wake ngati udzu,
Ndiponso kuti aziyala chiguduli pabedi lake nʼkuwazapo phulusa?
Kodi kumeneku nʼkumene mumati kusala kudya komanso tsiku losangalatsa kwa Yehova?
-