Yesaya 58:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndimafunanso kuti muzigawira chakudya chanu anthu anjala,+Kuti muziitanira mʼnyumba zanu anthu osauka ndi osowa pokhala,Kuti mukaona munthu wamaliseche muzimuveka+Ndiponso kuti musamadzibise kwa abale anu. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 58:7 Yesaya 2, ptsa. 281-282
7 Ndimafunanso kuti muzigawira chakudya chanu anthu anjala,+Kuti muziitanira mʼnyumba zanu anthu osauka ndi osowa pokhala,Kuti mukaona munthu wamaliseche muzimuveka+Ndiponso kuti musamadzibise kwa abale anu.