-
Yesaya 58:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Pa nthawiyo mudzaitana ndipo Yehova adzayankha.
Mudzafuula popempha thandizo ndipo iye adzanena kuti, ‘Ndikumva lankhulani!’
-