Yesaya 58:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova azidzakutsogolerani nthawi zonseNdipo adzakupatsani zinthu zofunika ngakhale mʼdziko louma.+Iye adzalimbitsa mafupa anuNdipo inu mudzakhala ngati dimba lothiriridwa bwino,+Ndiponso ngati kasupe amene madzi ake saphwera. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 58:11 Yesaya 2, ptsa. 284-285
11 Yehova azidzakutsogolerani nthawi zonseNdipo adzakupatsani zinthu zofunika ngakhale mʼdziko louma.+Iye adzalimbitsa mafupa anuNdipo inu mudzakhala ngati dimba lothiriridwa bwino,+Ndiponso ngati kasupe amene madzi ake saphwera.