Yesaya 59:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Dzanja la Yehova silinafupike moti nʼkulephera kupulumutsa,+Komanso khutu lake silinagonthe* moti nʼkulephera kumva.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 59:1 Yesaya 2, ptsa. 290-291 Nsanja ya Olonda,12/15/1987, tsa. 22
59 Dzanja la Yehova silinafupike moti nʼkulephera kupulumutsa,+Komanso khutu lake silinagonthe* moti nʼkulephera kumva.+