Yesaya 59:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ayi si choncho. Koma zolakwa zanu nʼzimene zakulekanitsani ndi Mulungu wanu.+ Machimo anu ndi amene amuchititsa kuti akubisireni nkhope yake,Ndipo sakufuna kumva zimene mukunena.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 59:2 Yesaya 2, ptsa. 290-291
2 Ayi si choncho. Koma zolakwa zanu nʼzimene zakulekanitsani ndi Mulungu wanu.+ Machimo anu ndi amene amuchititsa kuti akubisireni nkhope yake,Ndipo sakufuna kumva zimene mukunena.+