Yesaya 59:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nʼchifukwa chake chilungamo chatitalikira kwambiri,Ndipo zinthu zolungama sizikutipeza. Tikuyembekezera kuwala, koma mʼmalomwake tikungoona mdima.Tikuyembekezera tsiku lowala, koma tikupitirizabe kuyenda mumdima waukulu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 59:9 Yesaya 2, ptsa. 294-295
9 Nʼchifukwa chake chilungamo chatitalikira kwambiri,Ndipo zinthu zolungama sizikutipeza. Tikuyembekezera kuwala, koma mʼmalomwake tikungoona mdima.Tikuyembekezera tsiku lowala, koma tikupitirizabe kuyenda mumdima waukulu.+