Yesaya 59:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tikungopapasa khoma ngati anthu amene ali ndi vuto losaona,Tikungopapasapapasa ngati anthu opanda maso.+ Tikupunthwa masanasana ngati kuti tili mumdima wamadzulo.Pakati pa anthu amphamvu tikungokhala ngati anthu akufa. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 59:10 Yesaya 2, ptsa. 294-295
10 Tikungopapasa khoma ngati anthu amene ali ndi vuto losaona,Tikungopapasapapasa ngati anthu opanda maso.+ Tikupunthwa masanasana ngati kuti tili mumdima wamadzulo.Pakati pa anthu amphamvu tikungokhala ngati anthu akufa.