-
Yesaya 59:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Tonsefe tikungolira ngati zimbalangondo
Ndipo tikungokhalira kubuula momvetsa chisoni ngati njiwa.
Tikuyembekezera chilungamo koma sichikupezeka.
Tikuyembekezera chipulumutso koma chili kutali ndi ife.
-