Yesaya 59:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa zolakwa zathu zachuluka pamaso panu,+Tchimo lathu lililonse likupereka umboni wotsutsana nafe.+ Zolakwa zathu zili pa ife,Ndipo zochimwa zathu tikuzidziwa bwino.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 59:12 Yesaya 2, tsa. 295
12 Chifukwa zolakwa zathu zachuluka pamaso panu,+Tchimo lathu lililonse likupereka umboni wotsutsana nafe.+ Zolakwa zathu zili pa ife,Ndipo zochimwa zathu tikuzidziwa bwino.+