Yesaya 59:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chilungamo chabwezedwa mʼmbuyo,+Ndipo chilungamocho chaima patali.+Chifukwa choonadi chapunthwa* mʼbwalo lamumzinda,Ndipo zinthu zolungama zikulephera kulowamo. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 59:14 Yesaya 2, ptsa. 295-297
14 Chilungamo chabwezedwa mʼmbuyo,+Ndipo chilungamocho chaima patali.+Chifukwa choonadi chapunthwa* mʼbwalo lamumzinda,Ndipo zinthu zolungama zikulephera kulowamo.