Yesaya 59:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choonadi chasowa*+Ndipo aliyense wokana kuchita zoipa akulandidwa zinthu zake. Yehova anaona zimenezi ndipo sanasangalale nazo,*Chifukwa panalibe chilungamo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 59:15 Yesaya 2, ptsa. 295-297
15 Choonadi chasowa*+Ndipo aliyense wokana kuchita zoipa akulandidwa zinthu zake. Yehova anaona zimenezi ndipo sanasangalale nazo,*Chifukwa panalibe chilungamo.+