Yesaya 59:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye ataona kuti panalibe munthu aliyense woti nʼkuthandizapo,Anadabwa kwambiri kuti palibe amene akulowererapo.Choncho anapulumutsa anthu* ndi dzanja lake,Ndipo chilungamo chake nʼchimene chinamulimbikitsa kuchita zimenezo. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 59:16 Yesaya 2, tsa. 297
16 Iye ataona kuti panalibe munthu aliyense woti nʼkuthandizapo,Anadabwa kwambiri kuti palibe amene akulowererapo.Choncho anapulumutsa anthu* ndi dzanja lake,Ndipo chilungamo chake nʼchimene chinamulimbikitsa kuchita zimenezo.