17 Choncho iye anavala chilungamo ngati chovala chamamba achitsulo,
Ndiponso anavala chipewa cha chipulumutso kumutu kwake.+
Anavala chilungamo ngati chovala kuti apereke chilango kwa adani ake+
Ndipo kuchita zinthu modzipereka kwambiri kunali ngati chovala chake chodula manja.