Yesaya 59:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye adzawapatsa mphoto chifukwa cha zimene achita:+ Adani ake adzawapatsa mkwiyo ndipo anthu otsutsana naye adzawapatsa chilango.+ Ndipo zilumba adzazipatsa chilango chogwirizana ndi zochita zawo. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 59:18 Yesaya 2, tsa. 298
18 Iye adzawapatsa mphoto chifukwa cha zimene achita:+ Adani ake adzawapatsa mkwiyo ndipo anthu otsutsana naye adzawapatsa chilango.+ Ndipo zilumba adzazipatsa chilango chogwirizana ndi zochita zawo.