-
Yesaya 59:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Amene ali kolowera dzuwa adzaopa dzina la Yehova,
Ndipo amene ali kotulukira dzuwa adzaopa ulemerero wake,
Chifukwa iye adzabwera ngati mtsinje wothamanga,
Umene ukuyendetsedwa ndi mzimu wa Yehova.
-