-
Yesaya 60:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Taona! Mdima udzaphimba dziko lapansi,
Ndipo mdima wandiweyani udzaphimba mitundu ya anthu.
Koma kuwala kwa Yehova kudzafika pa iwe,
Ndipo ulemerero wake udzaonekera pa iwe.
-