-
Yesaya 60:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Anthu onse a ku Sheba adzabwera.
Adzabwera atanyamula golide ndi lubani.
Iwo adzatamanda Yehova pamaso pa anthu onse.+
-