Yesaya 60:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nkhosa zonse za ku Kedara+ zidzasonkhanitsidwa kwa iwe. Nkhosa zamphongo za ku Nebayoti+ zidzakutumikira. Ine ndidzazilandira paguwa langa lansembe,+Ndipo ndidzakongoletsa nyumba yanga yaulemerero.*+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 60:7 Nsanja ya Olonda,7/1/2002, ptsa. 11-13 Yesaya 2, ptsa. 308, 310-311
7 Nkhosa zonse za ku Kedara+ zidzasonkhanitsidwa kwa iwe. Nkhosa zamphongo za ku Nebayoti+ zidzakutumikira. Ine ndidzazilandira paguwa langa lansembe,+Ndipo ndidzakongoletsa nyumba yanga yaulemerero.*+