Yesaya 60:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi amene akubwera akuuluka ngati mtambowa ndi ndani? Ndi ndani amene akubwera ngati nkhunda zimene zikuulukira mʼmakola awo?* Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 60:8 Nsanja ya Olonda,7/1/2002, ptsa. 12-131/1/2000, tsa. 137/15/1992, tsa. 32 Yesaya 2, tsa. 309
8 Kodi amene akubwera akuuluka ngati mtambowa ndi ndani? Ndi ndani amene akubwera ngati nkhunda zimene zikuulukira mʼmakola awo?*