Yesaya 60:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ulemerero wa Lebanoni udzabwera kwa iwe.+Mtengo wa junipa,* mtengo wa ashi* ndiponso mtengo wa mkungudza zidzabwera pa nthawi imodzi,+Kuti zikongoletse malo anga opatulika,Ndipo ine ndidzalemekeza malo oikapo mapazi anga.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 60:13 Nsanja ya Olonda,7/15/2015, ptsa. 7-97/1/2002, ptsa. 14-158/15/1989, ptsa. 15-16, 203/1/1987, tsa. 32 Yesaya 2, ptsa. 314-315
13 Ulemerero wa Lebanoni udzabwera kwa iwe.+Mtengo wa junipa,* mtengo wa ashi* ndiponso mtengo wa mkungudza zidzabwera pa nthawi imodzi,+Kuti zikongoletse malo anga opatulika,Ndipo ine ndidzalemekeza malo oikapo mapazi anga.+
60:13 Nsanja ya Olonda,7/15/2015, ptsa. 7-97/1/2002, ptsa. 14-158/15/1989, ptsa. 15-16, 203/1/1987, tsa. 32 Yesaya 2, ptsa. 314-315