Yesaya 60:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ana a anthu amene ankakupondereza adzabwera nʼkudzagwada pamaso pako.Anthu onse amene ankakuchitira zachipongwe adzagwada pamapazi ako,Ndipo adzakutchula kuti mzinda wa Yehova,Ziyoni wa Woyera wa Isiraeli.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 60:14 Yesaya 2, tsa. 315 Nsanja ya Olonda,1/1/2000, tsa. 14
14 Ana a anthu amene ankakupondereza adzabwera nʼkudzagwada pamaso pako.Anthu onse amene ankakuchitira zachipongwe adzagwada pamapazi ako,Ndipo adzakutchula kuti mzinda wa Yehova,Ziyoni wa Woyera wa Isiraeli.+