Yesaya 60:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngakhale kuti ndinakusiya komanso anthu ankadana nawe ndipo palibe aliyense ankadutsa mwa iwe,+Ine ndidzachititsa kuti ukhale chinthu chimene anthu adzachitamanda mpaka kalekale,Ndiponso chinthu chosangalatsa ku mibadwo yonse.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 60:15 Nsanja ya Olonda,7/1/2002, tsa. 151/1/2000, tsa. 14 Yesaya 2, ptsa. 315-316
15 Ngakhale kuti ndinakusiya komanso anthu ankadana nawe ndipo palibe aliyense ankadutsa mwa iwe,+Ine ndidzachititsa kuti ukhale chinthu chimene anthu adzachitamanda mpaka kalekale,Ndiponso chinthu chosangalatsa ku mibadwo yonse.+