17 Mʼmalo mwa kopa ndidzabweretsa golide,
Mʼmalo mwa chitsulo ndidzabweretsa siliva,
Mʼmalo mwa mtengo ndidzabweretsa kopa,
Ndipo mʼmalo mwa miyala ndidzabweretsa chitsulo.
Ndidzaika mtendere kuti ukhale ngati okuyangʼanira,
Komanso chilungamo kuti chikhale ngati okupatsa ntchito.+