Yesaya 60:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Dzuwa silidzakhalanso lokuunikira masana,Ndipo mwezi sudzakuunikiranso.Chifukwa Yehova adzakhala kuwala kwako mpaka kalekale,+Ndipo Mulungu wako adzakhala kukongola kwako.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 60:19 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 309 Nsanja ya Olonda,7/1/2002, tsa. 18 Yesaya 2, ptsa. 318-319
19 Dzuwa silidzakhalanso lokuunikira masana,Ndipo mwezi sudzakuunikiranso.Chifukwa Yehova adzakhala kuwala kwako mpaka kalekale,+Ndipo Mulungu wako adzakhala kukongola kwako.+