-
Yesaya 60:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Wamngʼono adzasanduka anthu 1,000,
Ndipo wochepa adzasanduka mtundu wamphamvu.
Ineyo Yehova ndidzapangitsa kuti zimenezi zichitike mofulumira pa nthawi yake.”
-