Yesaya 61:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzasangalala kwambiri mwa Yehova. Ndidzasangalala mwa Mulungu wanga ndi mtima wanga wonse.+ Chifukwa iye wandiveka zovala zachipulumutso.+Wandiveka mkanjo wa chilungamo,*Ngati mkwati amene wavala nduwira yofanana ndi ya wansembe,+Ndiponso ngati mkwatibwi amene wavala zinthu zake zodzikongoletsera. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 61:10 Yesaya 2, tsa. 333 Chisungiko cha Padziko Lonse, tsa. 68
10 Ndidzasangalala kwambiri mwa Yehova. Ndidzasangalala mwa Mulungu wanga ndi mtima wanga wonse.+ Chifukwa iye wandiveka zovala zachipulumutso.+Wandiveka mkanjo wa chilungamo,*Ngati mkwati amene wavala nduwira yofanana ndi ya wansembe,+Ndiponso ngati mkwatibwi amene wavala zinthu zake zodzikongoletsera.