Yesaya 62:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Chifukwa cha Ziyoni sindidzakhala chete,+Ndipo chifukwa cha Yerusalemu sindidzakhala pheeMpaka kulungama kwake kutawala kwambiri,+Ndiponso mpaka chipulumutso chake chitakhala ngati muuni woyaka moto.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 62:1 Yesaya 2, ptsa. 335-337
62 Chifukwa cha Ziyoni sindidzakhala chete,+Ndipo chifukwa cha Yerusalemu sindidzakhala pheeMpaka kulungama kwake kutawala kwambiri,+Ndiponso mpaka chipulumutso chake chitakhala ngati muuni woyaka moto.+