Yesaya 62:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Mitundu ya anthu idzaona kulungama kwako mkazi iwe,+Ndipo mafumu onse adzaona ulemerero wako.+ Iwe udzapatsidwa dzina latsopano+Limene Yehova adzasankhe.* Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 62:2 Yesaya 2, ptsa. 337-338
2 “Mitundu ya anthu idzaona kulungama kwako mkazi iwe,+Ndipo mafumu onse adzaona ulemerero wako.+ Iwe udzapatsidwa dzina latsopano+Limene Yehova adzasankhe.*