Yesaya 62:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa mofanana ndi mmene mnyamata amakwatirira namwali,Ana ako aamuna adzakukwatira. Ngati mmene mkwati amasangalalira chifukwa cha mkwatibwi,Mulungu wako adzasangalala chifukwa cha iwe.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 62:5 Yesaya 2, ptsa. 340-341
5 Chifukwa mofanana ndi mmene mnyamata amakwatirira namwali,Ana ako aamuna adzakukwatira. Ngati mmene mkwati amasangalalira chifukwa cha mkwatibwi,Mulungu wako adzasangalala chifukwa cha iwe.+