Yesaya 62:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova walumbira atakweza dzanja lake lamanja ndiponso mkono wake wamphamvu kuti: “Sindidzaperekanso mbewu zanu kwa adani anu kuti chikhale chakudya chawo,Ndipo alendo sadzamwa vinyo wanu watsopano amene munamupeza movutikira.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 62:8 Yesaya 2, ptsa. 344-345
8 Yehova walumbira atakweza dzanja lake lamanja ndiponso mkono wake wamphamvu kuti: “Sindidzaperekanso mbewu zanu kwa adani anu kuti chikhale chakudya chawo,Ndipo alendo sadzamwa vinyo wanu watsopano amene munamupeza movutikira.+