Yesaya 62:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dutsani mʼmageti, dutsani mʼmageti. Lambulani njira kuti anthu adutse.+ Konzani msewu, konzani msewu waukulu. Muchotsemo miyala.+ Anthu a mitundu yosiyanasiyana muwakwezere chizindikiro+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 62:10 Nsanja ya Olonda,6/15/2014, tsa. 3 Yesaya 2, ptsa. 345-346
10 Dutsani mʼmageti, dutsani mʼmageti. Lambulani njira kuti anthu adutse.+ Konzani msewu, konzani msewu waukulu. Muchotsemo miyala.+ Anthu a mitundu yosiyanasiyana muwakwezere chizindikiro+