Yesaya 63:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nʼchifukwa chiyani zovala zanu zili zofiira,Ndipo nʼchifukwa chiyani zovala zanu zikuoneka ngati za munthu woponda mphesa mʼchoponderamo mphesa?+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 63:2 Yesaya 2, ptsa. 352-353
2 Nʼchifukwa chiyani zovala zanu zili zofiira,Ndipo nʼchifukwa chiyani zovala zanu zikuoneka ngati za munthu woponda mphesa mʼchoponderamo mphesa?+