Yesaya 63:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye anati: “Ndithu awa ndi anthu anga, ana amene sadzachita zosakhulupirika.”*+ Choncho iye anakhala Mpulumutsi wawo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 63:8 Yesaya 2, ptsa. 354-356
8 Iye anati: “Ndithu awa ndi anthu anga, ana amene sadzachita zosakhulupirika.”*+ Choncho iye anakhala Mpulumutsi wawo.+