Yesaya 63:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma iwo anapanduka+ nʼkumvetsa chisoni mzimu wake woyera.+ Kenako iye anakhala mdani wawo,+Ndipo anachita nawo nkhondo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 63:10 Yesaya 2, ptsa. 356-357
10 Koma iwo anapanduka+ nʼkumvetsa chisoni mzimu wake woyera.+ Kenako iye anakhala mdani wawo,+Ndipo anachita nawo nkhondo.+