Yesaya 63:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mofanana ndi ziweto zimene zatsetserekera kuchigwa,Mzimu wa Yehova unawachititsa kuti apume.”+ Izi ndi zimene munachita potsogolera anthu anu,Kuti mudzipangire dzina laulemerero.*+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 63:14 Yesaya 2, ptsa. 357-358
14 Mofanana ndi ziweto zimene zatsetserekera kuchigwa,Mzimu wa Yehova unawachititsa kuti apume.”+ Izi ndi zimene munachita potsogolera anthu anu,Kuti mudzipangire dzina laulemerero.*+