-
Yesaya 63:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Kwa nthawi yaitali, takhala ngati anthu amene simunawalamulirepo,
Ngati anthu amene sanadziwikepo ndi dzina lanu.
-