Yesaya 64:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tonse takhala ngati munthu wodetsedwa,Ndipo zochita zathu zonse zolungama zili ngati kansalu kamene mkazi amavala pa nthawi yosamba.+ Tonsefe tidzanyala ngati tsamba,Ndipo zolakwa zathu zidzatiuluzira kutali ngati mphepo. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 64:6 Nsanja ya Olonda,1/15/2007, tsa. 11 Yesaya 2, tsa. 365
6 Tonse takhala ngati munthu wodetsedwa,Ndipo zochita zathu zonse zolungama zili ngati kansalu kamene mkazi amavala pa nthawi yosamba.+ Tonsefe tidzanyala ngati tsamba,Ndipo zolakwa zathu zidzatiuluzira kutali ngati mphepo.