Yesaya 64:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Palibe amene akutchula dzina lanu popemphera,Palibe amene akuyesetsa kuti mumuthandize,Mwatibisira nkhope yanu,+Ndipo mwatichititsa kuti tikumane ndi mavuto* chifukwa cha zolakwa zathu. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 64:7 Yesaya 2, ptsa. 365-368
7 Palibe amene akutchula dzina lanu popemphera,Palibe amene akuyesetsa kuti mumuthandize,Mwatibisira nkhope yanu,+Ndipo mwatichititsa kuti tikumane ndi mavuto* chifukwa cha zolakwa zathu.