Yesaya 65:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu amene amandikhumudwitsa nthawi zonse mopanda manyazi,+Amene amapereka nsembe mʼminda+ komanso kufukiza nsembe zautsi panjerwa. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 65:3 Yesaya 2, ptsa. 374-375
3 Anthu amene amandikhumudwitsa nthawi zonse mopanda manyazi,+Amene amapereka nsembe mʼminda+ komanso kufukiza nsembe zautsi panjerwa.