Yesaya 65:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa cha zolakwa zawo komanso zolakwa za makolo awo,”+ akutero Yehova. “Chifukwa choti afukiza nsembe zautsi pamapiriNdipo andinyoza pazitunda,+Ine ndiwayezera malipiro awo onse choyamba.”* Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 65:7 Yesaya 2, ptsa. 375-376
7 Chifukwa cha zolakwa zawo komanso zolakwa za makolo awo,”+ akutero Yehova. “Chifukwa choti afukiza nsembe zautsi pamapiriNdipo andinyoza pazitunda,+Ine ndiwayezera malipiro awo onse choyamba.”*