Yesaya 65:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova wanena kuti: “Munthu angathe kugwiritsa ntchito phava la mphesa popanga vinyo watsopanoNdipo wina amanena kuti, ‘Musaliwononge, chifukwa muli zinthu zabwino* mmenemu.’ Inenso ndidzachita zofanana ndi zimenezi chifukwa cha atumiki anga,Sindidzawawononga onse.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 65:8 Yesaya 2, ptsa. 376-377
8 Yehova wanena kuti: “Munthu angathe kugwiritsa ntchito phava la mphesa popanga vinyo watsopanoNdipo wina amanena kuti, ‘Musaliwononge, chifukwa muli zinthu zabwino* mmenemu.’ Inenso ndidzachita zofanana ndi zimenezi chifukwa cha atumiki anga,Sindidzawawononga onse.+