Yesaya 65:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma inu muli mʼgulu la anthu amene asiya Yehova,+Anthu amene aiwala phiri langa loyera,+Amene amayalira tebulo mulungu wa Mwayi,Komanso amene amadzaza makapu ndi vinyo wosakaniza nʼkupereka kwa mulungu wa Zokonzedweratu. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 65:11 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 44 Nsanja ya Olonda,6/1/2006, tsa. 27 Yesaya 2, ptsa. 377-379 Galamukani!,8/8/1994, tsa. 216/8/1992, tsa. 11
11 Koma inu muli mʼgulu la anthu amene asiya Yehova,+Anthu amene aiwala phiri langa loyera,+Amene amayalira tebulo mulungu wa Mwayi,Komanso amene amadzaza makapu ndi vinyo wosakaniza nʼkupereka kwa mulungu wa Zokonzedweratu.
65:11 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 44 Nsanja ya Olonda,6/1/2006, tsa. 27 Yesaya 2, ptsa. 377-379 Galamukani!,8/8/1994, tsa. 216/8/1992, tsa. 11