Yesaya 65:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Atumiki anga adzadya, koma inu mudzakhala ndi njala.+ Atumiki anga adzamwa,+ koma inu mudzakhala ndi ludzu. Atumiki anga adzasangalala,+ koma inu mudzachita manyazi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 65:13 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 234-235 Yesaya 2, ptsa. 379-380
13 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Atumiki anga adzadya, koma inu mudzakhala ndi njala.+ Atumiki anga adzamwa,+ koma inu mudzakhala ndi ludzu. Atumiki anga adzasangalala,+ koma inu mudzachita manyazi.+